Khasu lake linali lalifupi kwambiri.
His hoe was too short.
Khomo lake linali lalifupi kwambiri.
His doorway was too low.
Bedi/kama lake linali yalifupi kwambiri.
His bed was too short.
Njinga lake linali yalifupi kwambiri.
His bicycle was too short.
Bambo uyu anali wam’tali kwambiri.
This man was too tall!
Anapanga chogwilila khasu chachitali.
He made a very long hoe handle.
Anapanga khomo lake kukhala yaitali kwambiri.
He made very high door frames.
Anapanga bedi/kama yaitali kwambiri.
He made a very long bed.
Anagula njinga yaitali kwambiri.
He bought a very high bicycle.
Anakhala pa m’pando wautali kwambiri. Anadya ndi foloko yaitali kwambiri.
He sat on a very high chair. He ate with a very long fork.
Anachoka panyumba yake ndipo anakhala ku thengo lalikulu. Anakhala kwa zaka zambiri.
He left his house and lived in a big forest. He lived for many years.