Uyu ndi Khalai. Ali ndi zaka zisanu ndi ziwiri. Dzina lake litanthauza kuti “wabwino” mucilankhulo chake, Lubukusu.
这是卡莱。她今年七岁。在肯尼亚当地方言里,这个名字是“美好事物”的意思。
Khalai amauka ndikukmba ndi mtengo wa malalanje. “Chonde, mtengo wamalalanje, kula ndipo utipatse malalanje ambiri akupsya”.
卡莱早上醒来,跟橙子树说:“橙子树啊橙子树,快点长大吧,给我们结好多又大又甜的橙子!”
Khali ayenda ku sukulu. Pa njira, akamba ndi msipu. “Chonde, kula msipu ndikukhala obiliwira ndipo musaume.”
在卡莱走路去上学的路上,她对草地说:“草地啊草地,你一定要长得绿油油的,别干枯了。”
Khalai apita pa maluwa amthengo. “Chonde, maluwa, pitilizani kukula kuti ndikuikeni mu tsitsi langa.”.
卡莱路过了野花,她对野花说:“野花啊野花,你们尽情地开放吧,这样我可以把你们夹在我的头发里。”
Ku sukulu, Khalai akamba ndi mtengo pakati pa sukulu. “Chonde mtengo, khalani ndi nthambi zikulu kuti tiziwerengera pa pansi pa mtengo.
在学校,卡莱对操场中间的树说:“小树啊小树,快点长出枝叶吧,这样我们就可以在树荫里读书了。”
Khalai akamba ndi chitseko chakusukulu. “Chonde, kulani olimba ndiponso osalola anthu oipa kti alowe.
卡莱还对学校附近的灌木丛说:“灌木啊灌木,你们一定要长得壮壮的,这样坏人就进不了学校了。”
Pamene Khalai abwelera kunyumba, ayendera mtengo walalanje. “Kodi malalanje ako apsya kale?”. Afunsa Khalai.
当卡莱从学校回到家里,她又去看了看橙子树,问它:“你结橙子了吗?”
Malalanje akalibe kupya,” anena Khalai. “Mwina, uzandikhalira ndi lalanje lakupya”.
卡莱叹了一口气:“橙子还是绿色的,我明天再来看看你吧!或许到了明天你就会给我一只又大又甜的橙子了。”