下载 PDF
返回故事列表

Mbuzi, Galu ndi Ng’ombe 山羊、野狗、和水牛

作者 Fabian Wakholi

插图 Marleen Visser, Ingrid Schechter

译文 David Sani Mwanza

配音 Christine Mwanza

语言 齐切瓦语

级别 2级

将整故事念出来 本故事尚未有语音版。


Mbuzi, Galu ndi Ng’ombe anali abwenzi kwambiri. Tsiku lina, anapita paulendo ndi galimoto.

山羊、野狗、和水牛是很要好的朋友。有一天,他们一起坐出租车。


Pamene anafika pothela pa ulendo wao, Mtekenya anawafunsa kuti alipile ndalama. Ng’ombe inalipila.

当他们到了目的地的时候,司机叫他们交车费。水牛把她自己的那份交了。


Galu analipila ndalama yopitilila chifukwa analibe ndalama yokwanila muyeso wa mtengo.

野狗没有带零钱,所以他就多给了一点儿。


Mtekenya anali pafupi kupasa Galu chenji yake pamene mbuzi inathawa kopanda kulipira.

司机正要找钱给野狗,没想到山羊没有给钱就跑掉了。


Mtekenya anakalipa kwambiri. Anayenda popanda kupasa Galu chenji yake.

司机很生气,结果他没有给野狗找钱就开走了。


Ndiye chifukwa chake,Galu amathangila galimoto kusonjera amene ali ndi chenji yake.

所以,现在你可以看到野狗看到车子就拼命追上去,因为他想叫司机给他找钱。


Mbuzi imathawa ikamvera galimoto. Imaopa kuti angaimangise chifukwa sanalipile mtekenya.

山羊呢,一听到有车来就吓得赶快逃走,因为她怕没交车费被人抓起来。


Ndipo Ng’ombe siimaikako nzelu ngati galimoto ili kubwela. Ng’ombe imayenda pang’ono pang’ono chifukwa adziwa kuti analipila ndalama mokwana.

可是水牛听到车来一点儿都不急。她不慌不忙地过马路,因为她知道她已经把她自己那份交了。


作者: Fabian Wakholi
插图: Marleen Visser, Ingrid Schechter
译文: David Sani Mwanza
配音: Christine Mwanza
语言: 齐切瓦语
级别: 2级
出处: 原文来自非洲故事书Goat, Dog and Cow
共享创意授权条款
本着作系采用共享创意 署名 3.0 未本地化版本授权条款授权。
选项
返回故事列表 下载 PDF