Ndimadzuka ndi kusonkha moto.
I wake up and make fire.
Ndimabvundula madzi yomwe ali pa moto.
I stir the pot.
Chifukwa nchyani ndimagwira ncthitomwaphanvu ine ndekha… Pamene mphyanga akonda kusewera chabe?
Why do I work so hard…
… when my brother is busy playing?