Mutima wanga umvela zinthu zambiri.
My heart feels a lot of
things.
Ndimvera kukondwera ngati ambuye atiuza nthano.
I feel happy when my
granny tells us stories
in the evening.
Ndimvera kukhala wopusa ngati ndisewera ndi mzanga.
I feel silly when I play
with my friend.
Ndimvera kukalipa ngati atate akamba kuti alibe ndalama.
I feel bad when my dad
says he does not have
money.
Ndimvera wokondewa ngati amai andikumbatira.
I feel loved when my
mom gives me a hug.