Regresar a lista de cuentos
Zama ndi wamkulu
¡Zama es genial!
Michael Oguttu
Vusi Malindi
Jessy Sakala
Christine Mwanza
El audio no está disponible actualmente.
M’ngono wanga amacedwa kugona. Ndimauka m’mamawa cifukwa ndine wamkulu!
Mi hermano pequeño se despierta muy tarde. Yo despierto temprano, ¡porque soy genial!
Ndine ndimalowetsa dzuwa.
Yo soy la que deja que la luz del sol entre a nuestra casa.
“Ndiwe nthanda yanga yam’mawa,” amatelo amai.
“Eres mi estrella mañanera,” dice mamá.
Ndimasamba ndekha masiku onse, sindifunanso thandizo iliyonse.
Me aseo sola y no necesito ayuda.
Ndingasambe ndi madzi odzidzila, ndi sopo wamtambo onunkhila.
Puedo soportar el agua fría y el jabón azul apestoso.
Amai amandikumbutsa, “osayiwala kutsuka mano.” Ndimawayanka kuti “ine ai, sindingaiwale ai!”
Mamá me dice, “No te olvides de los dientes.” Yo le respondo, “¡Nunca los olvido!”
Ndikasiliza kusamba, ndimapatsa moni agogo amuna ndi alongo a atate anga, ndimawafunila tsiku labwino.
Después de mi aseo, saludo a mi abuelo y a mi tía, y les deseo que tengan un buen día.
Kenaka ndimabvala ndekha. “Ndine wamkulu tsopano amama,” ndimanena.
Luego, me visto, “Ahora soy grande, mamá,” le digo.
Ndimanga mabatani komanso nthambo za nsapato ndekha.
Puedo abotonarme y abrochar mis zapatos.
Ndimayesetsa kuti mbale wanga adziwe nkhani zonse za kusukulu.
Y me aseguro que mi hermano pequeño sepa todas las noticias de la escuela.
Mukalasi ndimacita zonse zothekela munjila iliyonse.
En clases, doy lo mejor de mí en todos los sentidos.
Ndimacita zabwino zonsezi tsiku ndi tsiku. Koma cimene ndikondetsetsa kwambili ndi kusowela!
Todos los días hago estas cosas buenas. Pero lo que más me gusta hacer es ¡jugar, jugar y jugar!
Texto: Michael Oguttu
Ilustraciones: Vusi Malindi
Translated by: Jessy Sakala
Lectura en voz alta: Christine Mwanza