Njovu imozi ipita kukamwa madzi.
Ein Elefant will Wasser trinken.
Anyamalikiti awiri apita kukamwa madzi.
Zwei Giraffen wollen Wasser trinken.
Njati zitatu ndi mbalame zinai nazonso zipita kukamwa madzi.
Drei Büffel und vier Vögel wollen Wasser trinken.
Mphala zisanu ndi nguluwe zisanu ndi imozi zipita kumadzi.
Fünf Antilopen und sechs Warzenschweine laufen zum Wasser.
Mbizi zisanu ndi ziwiri zithamangira kumadzi.
Sieben Zebras galoppieren zum Wasser.
Acule asanu ndi atatu kudzanso nsomba zisanu ndi zinai zinyaya m’madzi.
Acht Frösche und neun Fische schwimmen im Wasser.
Mkango umozi walira. Afunanso kumwa madzi. Ndani amene aopa mkango?
Ein Löwe brüllt. Auch er will trinken. Wer hat Angst vorm Löwen?
Njovu imozi ikumwa madzi ndi mkango.
Ein Elefant trinkt mit dem Löwen Wasser.