Kodi ndizawerengera ndani?
Wem lese ich vor?
Kodi ndizawerengera ndani?
Wem lese ich vor?
Amai ndi agogo ndi otangwanika.
Meine Mutter und Oma sind beschäftigt.
Kodi ndizawerengera ndani?
Wem lese ich vor?
Atate ndi asukulu ndi otangwanika.
Mein Vater und Opa sind beschäftigt.
Kodi ndizawerengera ndani? Ndingaziwerengere ndekha!
Wem lese ich vor? Ich lese mir selbst vor!