Mutima wanga umvela zinthu zambiri.
Mein Herz fühlt viele Dinge.
Ndimvera kukondwera ngati ambuye atiuza nthano m’madzulo.
Ich fühle mich glücklich, wenn Oma uns am Abend Geschichten erzählt.
Ndimvera kukhala wosangalala ngati ndisewera ndi mzanga.
Ich fühle mich albern, wenn ich mit meiner Freundin spiele.
Ndimamvera kuipa ngati atate anena kuti alibe ndalama.
Ich fühle mich schlecht, wenn mein Papa sagt, dass er kein Geld hat.
Ndimvera wokondedwa ngati amai andikumbatira.
Ich fühle mich geliebt, wenn meine Mama mich umarmt.