Ndimadzuka ndi kusonkha moto.
Je me réveille et j’allume un feu.
Ndimawilitsa madzi.
Je fais bouillir de l’eau.
Ndimadula nkhuni.
Je fends du bois de chauffage.
Chifukwa nciani ndimagwila ncthito mwaphamvu ine ndekha… Pamene mphwanga atangwanidwa ndi kusewela cabe?
Pourquoi est-ce que je travaille si fort… … quand mon frère est en train de jouer ?