Sakima anali kukhala ndi makolo ake ndi mlongo wake wa zaka zakubadwa zinai. Anakhala pa malo a munthu wolemela, Nyumba yao inali ya udzu pothela pa mzele wa mitengo.
萨可满和他的父母,还有四岁的妹妹住在一起,他们住在一个富人的土地上,他们的茅草屋在一排大树的后面。
Pamene Sakima anali ndi zaka zitatu, anadwala ndipo anakhala wa khungu. Sakima anali ndi matalanta.
萨可满三岁的时候,生了一场大病,从此,萨可满就看不见了,其实萨可满是一个非常有天赋的孩子。
Sakima anali kukwanitsa kuchita zinthu zambili zomwe ana a zaka zisanu ndi cimodzi sankakwanisa kuchita. Mwachisanzo, anali kukhala ndi anthu akalu a m’mudzi ndi kukamba zinthu zofunikila.
Makolo a Sakima anali kusewenza pa nyumba ya bambo wolemela. Anachoka panyumba m’mamawa ndi kubwelela kunyumba mumadzulo mocedwa. Sakima anali kukhala ndi mlongo wake.
Sakima anasiliza kuimba nyimbo yake ndipo anatembenuka kufuna kubwelela kunyumba. Koma bambo wolemela anatuluka naumuuza nati, “Chonde, imbanso nyimbo.”
萨可满唱完了,准备离开。富人跑出来,说:“请再唱一遍吧!”
Pa nthawi yomweyo, amuna awili anabwela apo anyamula munthu. Anali anapeza mwana wa bambo wolemelayo atamenyedwa ndi kusiyidwa pambali pa mseu.
就在那时,两个人抬着担架走来了,担架上是富人的儿子!他们发现这个人被打得面目全非,躺在路边。
Bambo wolemela anakondwela kwambili kuona mwana wake. Anapatsa mphatso kwa Sakima powatonthoza. Anapeleka mwana wao ndi Sakima ku chipatala kuti Sakima akayambe kuonanso.