Kodi ndizawerengera ndani?
لِمَنْ سَأقْرَأُ؟
Kodi ndizawerengera ndani?
لِمَنْ سَأقْرَأُ؟
Amai ndi agogo ndi otangwanika.
أُمِّي وَجَدَّتِي مَشْغُولَتَانِ.
Kodi ndizawerengera ndani?
لِمَنْ سَأقْرَأ؟
Atate ndi asukulu ndi otangwanika.
أَبِي وَجَدِّي مَشْغُولَانِ.
Kodi ndizawerengera ndani? Ndingaziwerengere!
لِمَنْ سَأقْرَأ؟ سَأَقْرَأُ لِنَفْسِي!