Mutima wanga umvela zinthu zambili.
Mi corazón siente muchas cosas.
Ndimvela kukondwela ngati ambuya anga atiuza nthano m’madzulo.
Me siento feliz cuando mi abuelita me cuenta cuentos en las tardes.
Ndimvela kukhala wosangalala ngati ndisewela ndi mzanga.
Me siento chistosa cuando juego con mis amigos.
Ndimamvela kuipa ngati atate anena kuti alibe ndalama.
Me siento mal cuando mi papá me dice que no tiene dinero.
Ndimvela wokondedwa ngati amai anga andikumbatila.
Me siento querida cuando mi mamá me da un abrazo.