kodi ali panyasi pa kama(bedi)?
¿Estará debajo de la cama?
Kodi ali pamwamba pa kabati?
¿Estará encima del armario?
kodi ali kumbuyo kwa mpando?
¿Estará detrás del sofá?
Kodi ali pafupi ndi motaila zinyalala?
¿Estará al lado del bote de basura?
Kodi ali mkati mwa nswanda/dengo?
¿Estará dentro de la cesta?
Kodi ali pabwalo pa nyumba?
¿Estará afuera de la casa?