Ndimadzuka ndi kusonkha moto.
I wake up and make fire.
Je me réveille et j’allume un feu.
Ndimabwatutsa madzi.
I boil some water.
Je fais bouillir de l’eau.
Ndimadula nkhuni.
I chop the firewood.
Je fends du bois de chauffage.
Ndimabvundula madzi yomwe ali pa moto.
I stir the pot.
Je remue le chaudron.
Chifukwa nchyani ndimagwira ncthitomwaphanvu ine ndekha…
Pamene mphyanga akonda kusewera chabe?
Why do I work so hard…
… when my brother is busy playing?
Pourquoi est-ce que je travaille si fort… … quand mon frère est en train de jouer ?